Ezekieli 39:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Inu mudzakhuta patebulo langa. Mudzadya nyama ya mahatchi, ya okwera magaleta, ya anthu amphamvu ndi ankhondo a mitundu yosiyanasiyana,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
20 “‘Inu mudzakhuta patebulo langa. Mudzadya nyama ya mahatchi, ya okwera magaleta, ya anthu amphamvu ndi ankhondo a mitundu yosiyanasiyana,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+