Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 76:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Hatchi komanso wokwera galeta agona tulo tofa nato chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Mulungu wa Yakobo.+

  • Ezekieli 38:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndithu ine ndidzakubweza n’kukukola chibwano ndi ngowe.+ Kenako ndidzakukokera pafupi limodzi ndi gulu lako lonse lankhondo,+ mahatchi ako ndi asilikali ako okwera pamahatchi. Asilikali onsewa ndi ovala mwaulemerero.+ Iwo ndi khamu lalikulu lonyamula zishango zazikulu ndi zazing’ono, ndipo onsewo ndi aluso lomenya nkhondo pogwiritsa ntchito malupanga.+

  • Hagai 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndithu ndidzagonjetsa maufumu ndi kuchotsa mphamvu za maufumu a anthu a mitundu ina.+ Ndiwononga magaleta* ndi okwera pamagaletawo. Mahatchi* ndi okwera mahatchiwo adzaphedwa.+ Aliyense adzapha m’bale wake ndi lupanga.’”+

  • Chivumbulutso 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 kuti mudzadye minofu+ ya mafumu, ya akuluakulu a asilikali, ya amuna amphamvu,+ ya mahatchi+ ndi ya okwerapo ake, ndi minofu ya onse, ya mfulu ndi ya akapolo, ya olemekezeka ndi ya onyozeka.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena