-
Ezekieli 38:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ine ndidzakubweza nʼkukukola chibwano ndi ngowe.+ Kenako ndidzakupititsa kunkhondo limodzi ndi asilikali ako onse,+ mahatchi ako ndi amuna okwera pamahatchi ndipo onsewo adzavala mwaulemerero. Iwo adzakhala gulu lalikulu lonyamula zishango zazikulu ndi zazingʼono, ndipo onsewo ndi aluso lomenya nkhondo pogwiritsa ntchito malupanga.
-