2 Mafumu 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+ Ezekieli 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzakukola ndi ngowe munsagwada zako+ ndi kuchititsa nsomba za m’ngalande za mtsinje wa Nailo kukakamira kumamba ako. Ndidzakutulutsa m’ngalande za Nailo pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalandezo zimene zakakamira kumamba ako. Ezekieli 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakubweza ndi kukutsogolera.+ Ndidzakutenga kuchokera kumadera akutali kwambiri a kumpoto,+ n’kukubweretsa kumapiri a ku Isiraeli.
28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+
4 Ndidzakukola ndi ngowe munsagwada zako+ ndi kuchititsa nsomba za m’ngalande za mtsinje wa Nailo kukakamira kumamba ako. Ndidzakutulutsa m’ngalande za Nailo pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalandezo zimene zakakamira kumamba ako.
2 Ndidzakubweza ndi kukutsogolera.+ Ndidzakutenga kuchokera kumadera akutali kwambiri a kumpoto,+ n’kukubweretsa kumapiri a ku Isiraeli.