-
Ezekieli 38:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndithu ine ndidzakubweza n’kukukola chibwano ndi ngowe.+ Kenako ndidzakukokera pafupi limodzi ndi gulu lako lonse lankhondo,+ mahatchi ako ndi asilikali ako okwera pamahatchi. Asilikali onsewa ndi ovala mwaulemerero.+ Iwo ndi khamu lalikulu lonyamula zishango zazikulu ndi zazing’ono, ndipo onsewo ndi aluso lomenya nkhondo pogwiritsa ntchito malupanga.+
-