Ezekieli 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Udzabwera kuchokera kumalo ako, kumadera akutali a kumpoto.+ Udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu. Anthuwo adzakhala khamu lalikulu, adzakhala chigulu chachikulu chankhondo. Onsewo adzabwera atakwera pamahatchi.+
15 Udzabwera kuchokera kumalo ako, kumadera akutali a kumpoto.+ Udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu. Anthuwo adzakhala khamu lalikulu, adzakhala chigulu chachikulu chankhondo. Onsewo adzabwera atakwera pamahatchi.+