2 Mafumu 19:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adzabwerera kudzera njira imene anadutsa pobwera, ndipo sadzalowa mumzinda uno, ndiwo mawu a Yehova.+ Yesaya 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga.+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+
33 Adzabwerera kudzera njira imene anadutsa pobwera, ndipo sadzalowa mumzinda uno, ndiwo mawu a Yehova.+
29 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga.+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+