Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+

      Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+

      Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+

  • Salimo 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 N’chifukwa chiyani woipa amanyoza Mulungu?+

      Mumtima mwake amati: “Simudzandiimba mlandu.”+

  • Salimo 46:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.

      Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+

  • Yesaya 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kodi nkhwangwa ingadzikuze kuposa munthu amene akuigwiritsa ntchito? Kapena kodi chochekera matabwa chingadzikweze kuposa munthu amene akuchigwiritsa ntchito? Kodi chikwapu chinganyamule munthu amene wachinyamula m’mwamba, ndiponso kodi ndodo inganyamule m’mwamba munthu amene si mtengo?+

  • Yesaya 37:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+

      Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+

      Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+

      Ndi Woyera wa Isiraeli!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena