Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 83:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Pakuti ndi mtima wonse, iwo amagawana nzeru,+

      Ndipo anapangana pangano lotsutsana ndi inu.+

  • Yohane 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 kuti onse alemekeze Mwana+ monga mmene amalemekezera Atate. Wosalemekeza Mwana salemekeza Atate amene anamutuma.+

  • Yohane 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndikanapanda kuchita pakati pawo ntchito zimene wina aliyense sanachitepo,+ akanakhala opanda tchimo,+ koma tsopano aona ndipo adana nane, ndi kudananso ndi Atate wanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena