Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Miyambo 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pali m’badwo umene maso ake ali pamwamba kwambiri, ndiponso umene maso ake owala ali odzikweza.+