Salimo 101:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+Ndimamukhalitsa chete.+Sindingathe kupirira zochita za+Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+ Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Miyambo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Maso odzikweza ndi mtima wodzikuza+ ndizo nyale ya anthu oipa, ndipo zimenezi ndi tchimo.+ Yesaya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+ 2 Atesalonika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi wotsutsa+ amene amadzikweza pamwamba pa aliyense wotchedwa “mulungu” kapena chilichonse chopembedzedwa, moti amakhala pansi m’kachisi wa Mulungu, n’kumadzionetsera ngati mulungu.+
5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+Ndimamukhalitsa chete.+Sindingathe kupirira zochita za+Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+
11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+
4 Iye ndi wotsutsa+ amene amadzikweza pamwamba pa aliyense wotchedwa “mulungu” kapena chilichonse chopembedzedwa, moti amakhala pansi m’kachisi wa Mulungu, n’kumadzionetsera ngati mulungu.+