Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Salimo 50:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Umakhala pansi ndi kunenera m’bale wako zinthu zoipa,+Umapezera zifukwa mwana wamwamuna wa mayi ako.+ Miyambo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Woyenda uku ndi uku n’kumanena zoipa za anthu ena amaulula zinsinsi,+ ndipo usamagwirizane ndi munthu wotengeka ndi milomo yake.+ Tito 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chimodzimodzinso akazi achikulire.+ Akhale ndi khalidwe loyenera anthu opembedza. Asakhale amiseche,+ kapena akapolo a vinyo wambiri, koma akhale aphunzitsi a zinthu zabwino,
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.
20 Umakhala pansi ndi kunenera m’bale wako zinthu zoipa,+Umapezera zifukwa mwana wamwamuna wa mayi ako.+
19 Woyenda uku ndi uku n’kumanena zoipa za anthu ena amaulula zinsinsi,+ ndipo usamagwirizane ndi munthu wotengeka ndi milomo yake.+
3 Chimodzimodzinso akazi achikulire.+ Akhale ndi khalidwe loyenera anthu opembedza. Asakhale amiseche,+ kapena akapolo a vinyo wambiri, koma akhale aphunzitsi a zinthu zabwino,