Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye sanena miseche ndi lilime lake.+

      Sachitira mnzake choipa,+

      Ndipo satonza bwenzi lake lapamtima.+

  • Miyambo 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Amene amayendayenda n’kumanenera ena zoipa+ amaulula zinsinsi za anzake,+ koma wokhulupirika* amabisa nkhani.+

  • 1 Timoteyo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+

  • 2 Timoteyo 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 osakonda achibale awo,+ osafuna kugwirizana ndi anzawo,+ onenera anzawo zoipa,+ osadziletsa, oopsa,+ osakonda zabwino,+

  • Tito 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chimodzimodzinso akazi achikulire.+ Akhale ndi khalidwe loyenera anthu opembedza. Asakhale amiseche,+ kapena akapolo a vinyo wambiri, koma akhale aphunzitsi a zinthu zabwino,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena