Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Salimo 101:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+Ndimamukhalitsa chete.+Sindingathe kupirira zochita za+Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.
5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+Ndimamukhalitsa chete.+Sindingathe kupirira zochita za+Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+