Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Amunawo anayankha kuti: “Tikadzapanda kusunga lonjezo lathu, ifeyo tidzafe m’malo mwa inu!+ Mukasunga chinsinsi cha nkhaniyi, Yehova akadzatipatsa dziko lino, ifenso tidzakusonyezani kukoma mtima kosatha, ndipo tidzakhulupirika kwa inu.”+

  • Yoswa 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndipo ngati ungaulule nkhaniyi,+ tidzakhalanso opanda mlandu pa pangano limene watilumbiritsali.”

  • Yeremiya 38:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Patapita nthawi, akalonga onse anafika kwa Yeremiya ndipo anayamba kumufunsa mafunso. Yeremiya anawayankha mogwirizana ndi mawu onsewa amene mfumu inamulamula.+ Choncho akalongawo anakhala chete pamaso pake chifukwa sanamve zimene anakambirana.

  • Mateyu 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma mwamuna wake Yosefe, pokhala munthu wolungama ndiponso posafuna kumuchititsa manyazi kwa anthu,+ anaganiza zomusiya+ mwamseri.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena