Yoswa 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amunawo anayankha kuti: “Tikadzapanda kusunga lonjezo lathu, ifeyo tidzafe m’malo mwa inu!+ Mukasunga chinsinsi cha nkhaniyi, Yehova akadzatipatsa dziko lino, ifenso tidzakusonyezani kukoma mtima kosatha, ndipo tidzakhulupirika kwa inu.”+
14 Amunawo anayankha kuti: “Tikadzapanda kusunga lonjezo lathu, ifeyo tidzafe m’malo mwa inu!+ Mukasunga chinsinsi cha nkhaniyi, Yehova akadzatipatsa dziko lino, ifenso tidzakusonyezani kukoma mtima kosatha, ndipo tidzakhulupirika kwa inu.”+