Yoswa 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo amunawo atuluka usiku uno nthawi yotseka chipata+ itayandikira. Koma ine sindikudziwa kumene alowera. Fulumirani! Athamangireni! Muwapeza amenewo.” Salimo 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+
5 Ndipo amunawo atuluka usiku uno nthawi yotseka chipata+ itayandikira. Koma ine sindikudziwa kumene alowera. Fulumirani! Athamangireni! Muwapeza amenewo.”
39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+