Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Yobu anamuyankha kuti: “Ukulankhula ngati mmene amalankhulira akazi opusa.+ Kodi tizingolandira zabwino zokha kuchokera kwa Mulungu woona osalandiranso zoipa?”+ M’zonsezi Yobu sanachimwe ndi milomo yake.+

  • Salimo 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iye adzadula anthu onena kuti: “Ndi lilime lathu tidzapambana.+

      Timalankhula chilichonse chimene tikufuna ndi milomo yathu. Ndani angatilamulire?”

  • Miyambo 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Imfa ndiponso moyo zili mu mphamvu ya lilime,+ ndipo wolikonda adzadya zipatso zake.+

  • Yakobo 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena