Miyambo 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakamwa pa wolungama pamabala zipatso za nzeru,+ koma lilime lonena zopotoka lidzadulidwa.+ Miyambo 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zipatso za munthu wolungama ndizo mtengo wa moyo,+ ndipo munthu wopulumutsa miyoyo ndi wanzeru.+ Mateyu 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zotuluka m’kamwa zimachokera mumtima, ndipo zimenezo zimaipitsa munthu.+ Aefeso 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+ Yakobo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.
29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+
6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.