Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 14:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mboni yoona imapulumutsa anthu,+ koma mboni yonama imangonena bodza.+

  • Danieli 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.

  • Mateyu 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iye anawauza kuti: “Nditsatireni, ndipo ndikusandutsani asodzi a anthu.”+

  • Aroma 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Komabe, kodi angaitane bwanji munthu amene samukhulupirira?+ Angakhulupirire bwanji munthu amene sanamvepo za iye? Angamve bwanji za iye popanda wina kulalikira?+

  • 1 Akorinto 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Motero kwa Ayuda ndinakhala ngati Myuda,+ kuti ndipindule Ayuda. Kwa anthu otsatira chilamulo+ ndinakhala ngati wotsatira chilamulo+ kuti ndipindule anthu otsatira chilamulo, ngakhale kuti sindili pansi pa chilamulo.

  • Yakobo 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 dziwani kuti amene wabweza wochimwa panjira yake yoipa,+ adzapulumutsa moyo wa wochimwayo ku imfa+ ndipo adzakwirira machimo ambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena