Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 14:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mboni yokhulupirika ndi imene sinama,+ koma mboni yonyenga imanena bodza lokhalokha.+

  • 1 Timoteyo 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Zimenezi zidzachitikanso chifukwa cha chinyengo cha anthu olankhula mabodza,+ amene chikumbumtima chawo chili ngati chipsera+ chobwera chifukwa chopsa ndi chitsulo chamoto.

  • 2 Timoteyo 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anthu amenewa apatuka pa choonadi,+ ponena kuti kuuka kwa akufa kunachitika kale+ ndipo akuwononga chikhulupiriro cha ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena