Ekisodo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+ Miyambo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,+ ndipo wolankhula mabodza sadzapulumuka.+