Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Agalatiya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko, Yakobo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngati m’mitima mwanu muli nsanje yaikulu+ ndi kukonda mikangano,+ musadzitamande+ pakuti kutero n’kunamizira choonadi.+ 3 Yohane 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chake ndikadzabwera, ndidzaulula ntchito zake zimene akupitirizabe kuchita.+ Iye amatinenera zamwano,+ komanso chifukwa chosakhutira ndi zinthu zimenezi, iye salandira abalewo+ mwaulemu, ndipo amene amafuna kulandira+ abalewo, amawatsekereza+ ndi kuwachotsa+ mumpingo.
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.
20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,
14 Koma ngati m’mitima mwanu muli nsanje yaikulu+ ndi kukonda mikangano,+ musadzitamande+ pakuti kutero n’kunamizira choonadi.+
10 N’chifukwa chake ndikadzabwera, ndidzaulula ntchito zake zimene akupitirizabe kuchita.+ Iye amatinenera zamwano,+ komanso chifukwa chosakhutira ndi zinthu zimenezi, iye salandira abalewo+ mwaulemu, ndipo amene amafuna kulandira+ abalewo, amawatsekereza+ ndi kuwachotsa+ mumpingo.