Aefeso 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ m’bale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika mwa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+ Afilipi 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ine, mwa Ambuye Yesu ndikuyembekeza kutumiza Timoteyo kwa inu posachedwapa, kuti ndidzasangalale+ ndikadzamva mmene zinthu zilili kwa inu. Akolose 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tukiko,+ m’bale wanga wokondedwa komanso mtumiki wokhulupirika, ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakudziwitsani zonse za ine.
21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ m’bale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika mwa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+
19 Koma ine, mwa Ambuye Yesu ndikuyembekeza kutumiza Timoteyo kwa inu posachedwapa, kuti ndidzasangalale+ ndikadzamva mmene zinthu zilili kwa inu.
7 Tukiko,+ m’bale wanga wokondedwa komanso mtumiki wokhulupirika, ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakudziwitsani zonse za ine.