Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Deuteronomo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Deuteronomo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu akakonzera mnzake chiwembu mwa kupereka umboni wonama wakuti waphwanya lamulo,+ Salimo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sanena miseche ndi lilime lake.+Sachitira mnzake choipa,+Ndipo satonza bwenzi lake lapamtima.+
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.