Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+

  • 1 Mafumu 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako amuna awiri opanda pake anabwera n’kukhala patsogolo pa Naboti. Ndiyeno amuna opanda pakewo anayamba kupereka umboni wotsutsana ndi Naboti pamaso pa anthuwo, wakuti: “Naboti watemberera Mulungu ndi mfumu!”+ Pambuyo pake anamutulutsira kunja kwa mzindawo n’kumuponya miyala mpaka anafa.+

  • Salimo 27:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Musandipereke kwa adani anga.+

      Pakuti mboni zonama zandiukira,+

      Chimodzimodzinso munthu wachiwawa.+

  • Maliko 14:56
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 56 Ndipo anthu ambiri anali kupereka umboni wonama kutsutsana naye,+ koma maumboni awowo anali kutsutsana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena