Ekisodo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Deuteronomo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu akakonzera mnzake chiwembu mwa kupereka umboni wonama wakuti waphwanya lamulo,+ Salimo 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mboni zachiwawa zimaimirira.+Zimandifunsa zinthu zimene sindikudziwa.+ Miyambo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,+ ndipo wolankhula mabodza sadzapulumuka.+