1 Mafumu 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano usangomusiya, um’lange,+ poti ndiwe munthu wanzeru+ ndipo ukudziwa bwino zimene uyenera kumuchita. Utsitsire imvi zake+ ku Manda zili ndi magazi.”+ Miyambo 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mboni yonama idzawonongedwa,+ koma munthu amene amamvetsera adzalankhula kwamuyaya.+
9 Tsopano usangomusiya, um’lange,+ poti ndiwe munthu wanzeru+ ndipo ukudziwa bwino zimene uyenera kumuchita. Utsitsire imvi zake+ ku Manda zili ndi magazi.”+