Ekisodo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+ Deuteronomo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo oweruza azifufuza nkhaniyo mosamala.+ Mboniyo ikapezeka kuti ndi yonama ndipo yaneneza m’bale wake mlandu wonama, Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+ Miyambo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,+ ndipo wolankhula mabodza sadzapulumuka.+
23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+
18 Pamenepo oweruza azifufuza nkhaniyo mosamala.+ Mboniyo ikapezeka kuti ndi yonama ndipo yaneneza m’bale wake mlandu wonama,