Deuteronomo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 muzifunafuna, kufufuza ndi kufunsitsa za nkhani imeneyo.+ Mukapeza kuti ndi zoonadi, choipa chimenechi chachitikadi pakati panu, Deuteronomo 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo inu mwamva mutauzidwa, ndiponso mutafufuza mwatsimikizira kuti ndi zoona,+ chinthu choipachi chachitikadi mu Isiraeli, 2 Mbiri 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+ Yobu 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinali bambo weniweni kwa osauka,+Ndipo mlandu wa munthu amene sindinali kumudziwa ndinkaufufuza.+
14 muzifunafuna, kufufuza ndi kufunsitsa za nkhani imeneyo.+ Mukapeza kuti ndi zoonadi, choipa chimenechi chachitikadi pakati panu,
4 ndipo inu mwamva mutauzidwa, ndiponso mutafufuza mwatsimikizira kuti ndi zoona,+ chinthu choipachi chachitikadi mu Isiraeli,
6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+
16 Ndinali bambo weniweni kwa osauka,+Ndipo mlandu wa munthu amene sindinali kumudziwa ndinkaufufuza.+