Deuteronomo 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo inu mwamva mutauzidwa, ndiponso mutafufuza mwatsimikizira kuti ndi zoona,+ chinthu choipachi chachitikadi mu Isiraeli, Deuteronomo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ 1 Timoteyo 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usavomereze mlandu woneneza mkulu, kupatulapo ngati pali umboni wa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Aheberi 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu aliyense amene wanyalanyaza chilamulo cha Mose amafa popanda kumuchitira chifundo, ngati anthu awiri kapena atatu apereka umboni.+
4 ndipo inu mwamva mutauzidwa, ndiponso mutafufuza mwatsimikizira kuti ndi zoona,+ chinthu choipachi chachitikadi mu Isiraeli,
15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+
28 Munthu aliyense amene wanyalanyaza chilamulo cha Mose amafa popanda kumuchitira chifundo, ngati anthu awiri kapena atatu apereka umboni.+