Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+

  • Mateyu 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma akapanda kukumvera, upiteko ndi munthu wina mmodzi kapena awiri, kuti nkhani yonse ikatsimikizike ndi pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+

  • Mateyu 26:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 koma sanaupeze, ngakhale kuti kunabwera mboni zambiri zonama.+ Patapita nthawi, kunabwera mboni zina ziwiri

  • Yohane 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiponso m’Chilamulo chanu chomwechi analembamo kuti, ‘Umboni wa anthu awiri ndi woona.’+

  • 2 Akorinto 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Aka ndi kachitatu+ tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.”+

  • 1 Timoteyo 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Usavomereze mlandu woneneza mkulu, kupatulapo ngati pali umboni wa mboni ziwiri kapena zitatu.+

  • Aheberi 10:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Munthu aliyense amene wanyalanyaza chilamulo cha Mose amafa popanda kumuchitira chifundo, ngati anthu awiri kapena atatu apereka umboni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena