Deuteronomo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Yohane 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso m’Chilamulo chanu chomwechi analembamo kuti, ‘Umboni wa anthu awiri ndi woona.’+ 2 Akorinto 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aka ndi kachitatu+ tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.”+ 1 Timoteyo 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usavomereze mlandu woneneza mkulu, kupatulapo ngati pali umboni wa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Aheberi 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu aliyense amene wanyalanyaza chilamulo cha Mose amafa popanda kumuchitira chifundo, ngati anthu awiri kapena atatu apereka umboni.+
15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+
13 Aka ndi kachitatu+ tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.”+
28 Munthu aliyense amene wanyalanyaza chilamulo cha Mose amafa popanda kumuchitira chifundo, ngati anthu awiri kapena atatu apereka umboni.+