Numeri 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Aliyense wopezeka kuti wapha munthu,+ atatsimikiziridwa ndi mboni,+ aphedwe. Koma umboni wa munthu mmodzi si wokwanira kuti munthu aphedwe. Deuteronomo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Mateyu 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma akapanda kukumvera, upiteko ndi munthu wina mmodzi kapena awiri, kuti nkhani yonse ikatsimikizike ndi pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Yohane 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso m’Chilamulo chanu chomwechi analembamo kuti, ‘Umboni wa anthu awiri ndi woona.’+
30 “‘Aliyense wopezeka kuti wapha munthu,+ atatsimikiziridwa ndi mboni,+ aphedwe. Koma umboni wa munthu mmodzi si wokwanira kuti munthu aphedwe.
15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+
16 Koma akapanda kukumvera, upiteko ndi munthu wina mmodzi kapena awiri, kuti nkhani yonse ikatsimikizike ndi pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+