Numeri 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Aliyense wopezeka kuti wapha munthu,+ atatsimikiziridwa ndi mboni,+ aphedwe. Koma umboni wa munthu mmodzi si wokwanira kuti munthu aphedwe. Deuteronomo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthuyo aziphedwa mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Asaphedwe chifukwa cha umboni wa munthu mmodzi.+
30 “‘Aliyense wopezeka kuti wapha munthu,+ atatsimikiziridwa ndi mboni,+ aphedwe. Koma umboni wa munthu mmodzi si wokwanira kuti munthu aphedwe.
6 Munthuyo aziphedwa mutamva umboni wa pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+ Asaphedwe chifukwa cha umboni wa munthu mmodzi.+