Ekisodo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Deuteronomo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+ Miyambo 24:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Usakhale mboni yotsutsana ndi mnzako popanda umboni,+ chifukwa ukhoza kukhala wopusa ndi milomo yako.+ Yesaya 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wakhalidwe loipayo, njira zake n’zoipa.+ Iye amakonza zochita khalidwe lotayirira,+ n’cholinga choti apweteke anthu ozunzika pogwiritsa ntchito mawu abodza,+ ngakhale pamene munthu wosauka akunena zoona. Machitidwe 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kumeneko anabweretsa mboni zonama,+ zimene zinati: “Munthu uyu sakuleka kulankhula mawu onyoza malo oyera ano ndi Chilamulo.+
28 Usakhale mboni yotsutsana ndi mnzako popanda umboni,+ chifukwa ukhoza kukhala wopusa ndi milomo yako.+
7 Munthu wakhalidwe loipayo, njira zake n’zoipa.+ Iye amakonza zochita khalidwe lotayirira,+ n’cholinga choti apweteke anthu ozunzika pogwiritsa ntchito mawu abodza,+ ngakhale pamene munthu wosauka akunena zoona.
13 Kumeneko anabweretsa mboni zonama,+ zimene zinati: “Munthu uyu sakuleka kulankhula mawu onyoza malo oyera ano ndi Chilamulo.+