Yeremiya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Zili choncho, chifukwa pakati pa anthu anga papezeka anthu oipa.+ Iwo amawabisalira ndi kuwayang’anitsitsa ngati mmene wosaka mbalame amachitira.+ Awatchera msampha wowononga pakuti iwo amagwira anthu. Mika 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.
26 “‘Zili choncho, chifukwa pakati pa anthu anga papezeka anthu oipa.+ Iwo amawabisalira ndi kuwayang’anitsitsa ngati mmene wosaka mbalame amachitira.+ Awatchera msampha wowononga pakuti iwo amagwira anthu.
3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.