Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+ Miyambo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 N’zopanda phindu kuyala ukonde pamaso pa chilichonse chokhala ndi mapiko.+ Habakuku 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mdani amagwira zonsezi ndi mbedza+ ndipo amazikokolola ndi khoka lake n’kuzisonkhanitsa muukonde wake wophera nsomba.+ N’chifukwa chake iye amasangalala ndipo amakhala wokondwa.+
9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+
15 Mdani amagwira zonsezi ndi mbedza+ ndipo amazikokolola ndi khoka lake n’kuzisonkhanitsa muukonde wake wophera nsomba.+ N’chifukwa chake iye amasangalala ndipo amakhala wokondwa.+