Miyambo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti iwo sagona kufikira atachita zoipa.+ Tulo sitiwabwerera mpaka atakhumudwitsa wina.+ Yeremiya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mukhala wokwiya mpaka kalekale?* Kapena kodi muzingoyang’anira machimo athu mpaka muyaya?’+ Taona! Iwe wanena ndi kuchita zinthu zoipa ndipo wapambana.”+ Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+ Ezekieli 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwa iwetu muli atsogoleri+ a Isiraeli. Aliyense wa iwo akugwiritsa ntchito dzanja lake modzipereka kuti akhetse magazi.+
5 Kodi mukhala wokwiya mpaka kalekale?* Kapena kodi muzingoyang’anira machimo athu mpaka muyaya?’+ Taona! Iwe wanena ndi kuchita zinthu zoipa ndipo wapambana.”+
22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+
6 Mwa iwetu muli atsogoleri+ a Isiraeli. Aliyense wa iwo akugwiritsa ntchito dzanja lake modzipereka kuti akhetse magazi.+