Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Petulo 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+

  • Yuda 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu amenewa ali ngati miyala ikuluikulu yobisika m’madzi,+ pamene akudya nanu limodzi pa maphwando anu amene mumachita kuti musonyezane chikondi. Alinso ngati abusa amene amadzidyetsa okha mopanda mantha,+ mitambo yopanda madzi yotengeka+ ndi mphepo+ kupita uku ndi uku, mitengo yopanda zipatso koma nyengo yake yobereka zipatso ili pafupi kutha, yakufa kawiri, yozulidwa.+

  • Chivumbulutso 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena