Deuteronomo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Miyambo 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mboni yopanda pake imanyoza chilungamo,+ ndipo pakamwa pa anthu oipa pamameza zinthu zopweteka ena.+
28 Mboni yopanda pake imanyoza chilungamo,+ ndipo pakamwa pa anthu oipa pamameza zinthu zopweteka ena.+