Ekisodo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Ekisodo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+ Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Deuteronomo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu akakonzera mnzake chiwembu mwa kupereka umboni wonama wakuti waphwanya lamulo,+ Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+ Miyambo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,+ ndipo wolankhula mabodza sadzapulumuka.+
23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.