Miyambo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti iwo sagona kufikira atachita zoipa.+ Tulo sitiwabwerera mpaka atakhumudwitsa wina.+ Miyambo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti amadya mkate wa zoipa+ ndipo amamwa vinyo wachiwawa.+ Hoseya 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo akupindula ndi machimo a anthu anga, ndipo amalakalaka tchimo la anthuwo.+