Mika 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+ Chivumbulutso 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi+ a oyera, ndiponso magazi a mboni za Yesu.+ Nditamuona mkaziyo, ndinadabwa kwambiri.+
12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+
6 Ndipo ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi+ a oyera, ndiponso magazi a mboni za Yesu.+ Nditamuona mkaziyo, ndinadabwa kwambiri.+