Chivumbulutso 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atamatula chidindo chachisanu, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo+ ya amene anaphedwa+ chifukwa cha mawu a Mulungu, ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni+ imene anali nayo.
9 Atamatula chidindo chachisanu, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo+ ya amene anaphedwa+ chifukwa cha mawu a Mulungu, ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni+ imene anali nayo.