Mateyu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+ 1 Yohane 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+
9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+
12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+