Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 N’chifukwa chiyani anthu inu mukunyozabe nsembe zanga+ zimene ndinalamula m’nyumba yanga,+ n’kumalemekezabe ana anu koposa ine mwa kudzinenepetsa+ ndi mbali yabwino kwambiri ya nsembe iliyonse ya anthu anga Aisiraeli?+

  • Yesaya 56:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo ndi agalu adyera kwambiri+ ndipo sakhuta,+ komanso ndi abusa osamvetsa zinthu.+ Aliyense wa iwo wapatukira kunjira yake n’cholinga chopeza phindu lachinyengo lochokera m’dera lake.+ Iwo amati:

  • Mika 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena