Yeremiya 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndidzakuponyani kudziko limene mitima yanu idzalakalaka kubwererako, koma simudzabwererako.+ 2 Petulo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Popeza anasiya njira yowongoka, asocheretsedwa. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anakonda mphoto ya kuchita zoipa,+
15 Popeza anasiya njira yowongoka, asocheretsedwa. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anakonda mphoto ya kuchita zoipa,+