Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano iye anatumiza amithenga kwa Balamu,+ mwana wa Beori, ku Petori+ pafupi ndi Mtsinje*+ wa m’dziko lawo. Anawatuma kuti akamuitane, kuti: “Taonani! Anthu ochokera ku Iguputo afika kuno. Iwo adzaza dziko lino kulikonse kumene munthu angayang’ane,+ ndipo akukhala pafupi penipeni moyang’anana ndi ine.

  • Yuda 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+

  • Chivumbulutso 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena