Yoswa 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakati pa anthu amene ana a Isiraeli anawapha ndi lupanga, panali Balamu mwana wa Beori,+ wolosera zam’tsogolo+ uja. Yoswa 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+ 2 Petulo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Popeza anasiya njira yowongoka, asocheretsedwa. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anakonda mphoto ya kuchita zoipa,+ Yuda 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+
22 Pakati pa anthu amene ana a Isiraeli anawapha ndi lupanga, panali Balamu mwana wa Beori,+ wolosera zam’tsogolo+ uja.
9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+
15 Popeza anasiya njira yowongoka, asocheretsedwa. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anakonda mphoto ya kuchita zoipa,+
11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+